Atate athu

Atate athu muli m'mwamba,

dzina lanu liyeretsedwe,

ufumu wanu udze,

kufuna kwanu kuchitidwe,

monga kumwamba choncho pansi pano.

Mutipatse ife lero chakudya chathu cha lero.

Mutikhululukire ife zochimwa zathu monga

ifenso tiwakhululukira adani athu,

musatisiye ife m'chinyengo koma mutipulumutse ife ku zoyipa.

Amen.

Category:
Cinyanja